Salimo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+ Luka 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Pamenepo Ambuye ananena kuti: “Ndani kwenikweni amene ali mtumiki woyang’anira nyumba wokhulupirika+ ndi wanzeru,+ amene mbuye wake adzamuika kuyang’anira gulu la atumiki ake, kuti aziwapatsa chakudya chokwanira pa nthawi yake?+ 1 Akorinto 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Komanso pamenepa, chofunika kwa woyang’anira+ ndicho kukhala wokhulupirika.+
15 Inu Yehova, ndani amene angakhale mlendo m’chihema chanu?+Ndani angakhale m’phiri lanu lopatulika?+
42 Pamenepo Ambuye ananena kuti: “Ndani kwenikweni amene ali mtumiki woyang’anira nyumba wokhulupirika+ ndi wanzeru,+ amene mbuye wake adzamuika kuyang’anira gulu la atumiki ake, kuti aziwapatsa chakudya chokwanira pa nthawi yake?+