40 Iye anandiyankha kuti, ‘Yehova, amene ndakhala ndikuyenda pamaso pake movomerezeka,+ atumiza mngelo+ wake kuti apite nawe limodzi, ndipo ameneyo akakuthandiza ndithu kuti ukapeze chimene uyendere.+ Kumeneko, ukam’tengere mkazi mwana wanga, kwa abale anga, kubanja la bambo anga.+