Oweruza 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyi panali mwamuna wina wa ku Zora+ wa fuko la Dani,+ ndipo dzina lake anali Manowa.+ Mkazi wake anali wosabereka, moti analibe mwana.+ Oweruza 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patapita nthawi, mkaziyo anabereka mwana wamwamuna ndipo dzina lake anamutcha kuti Samisoni.+ Mnyamatayo anali kukula, ndipo Yehova anapitiriza kumudalitsa.+ Oweruza 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Samisoni anaweruza Isiraeli zaka 20 m’masiku a Afilisiti.+
2 Pa nthawiyi panali mwamuna wina wa ku Zora+ wa fuko la Dani,+ ndipo dzina lake anali Manowa.+ Mkazi wake anali wosabereka, moti analibe mwana.+
24 Patapita nthawi, mkaziyo anabereka mwana wamwamuna ndipo dzina lake anamutcha kuti Samisoni.+ Mnyamatayo anali kukula, ndipo Yehova anapitiriza kumudalitsa.+