Genesis 49:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Dani adzaweruza anthu a mtundu wake monga mmodzi wa mafuko a Isiraeli.+ Deuteronomo 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kwa Dani anati:+“Dani ndi mwana wa mkango.+Adzadumpha kuchokera ku Basana.”+ Yoswa 19:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Maere a 7+ anagwera fuko la ana a Dani+ potsata mabanja awo.