Genesis 49:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Dani adzakhala njoka yobisala m’mbali mwa msewu, njoka yokhala ndi tinyanga yobisala m’mphepete mwa njira, imene imaluma chidendene cha hatchi ndipo wokwerapo amagwa chagada.+ Deuteronomo 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kwa Dani anati:+“Dani ndi mwana wa mkango.+Adzadumpha kuchokera ku Basana.”+
17 Dani adzakhala njoka yobisala m’mbali mwa msewu, njoka yokhala ndi tinyanga yobisala m’mphepete mwa njira, imene imaluma chidendene cha hatchi ndipo wokwerapo amagwa chagada.+