Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 19:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Gawo la ana a Dani linawachepera,+ choncho anapita kukachita nkhondo ku Lesemu.+ Analanda mzindawo n’kupha anthu ake ndi lupanga. Kenako anautenga n’kuyamba kukhalamo ndipo anautcha Lesemu Dani, potengera dzina la kholo lawo Dani.+

  • Oweruza 18:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ana a Dani anatenga zimene Mika anapanga komanso wansembe+ wake, ndipo anapitiriza ulendo wawo wa ku Laisi+ kukaukira anthu aphee ndi osatekeseka.+ Atafika kumeneko anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kutentha mzindawo ndi moto.+

  • Oweruza 18:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Kuwonjezera apo, anatcha mzindawo kuti Dani, kutengera dzina la bambo awo lakuti Dani,+ amene anali wobadwa kwa Isiraeli.+ Ngakhale zili choncho, dzina loyamba la mzindawo linali Laisi.+

  • 1 Mbiri 12:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 A fuko la Dani, okafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo, analipo 28,600.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena