19 Iwo anamuyankha kuti: “Khala chete. Gwira pakamwa pako, ndipo upite nafe kuti ukakhale tate+ ndi wansembe+ wathu. Chabwino n’chiti, kuti upitirize kukhala wansembe m’nyumba ya munthu mmodzi,+ kapena kuti ukhale wansembe wa banja ndi fuko lonse mu Isiraeli?”+