Oweruza 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atatero Mika anamuuza kuti: “Ukhale ndi ine ndipo uzitumikira ngati tate+ ndi wansembe+ wanga. Ine ndizikupatsa ndalama zasiliva 10 pa chaka, komanso zovala zako zoyenera ndi chakudya.” Pamenepo Mleviyo analowa m’nyumbamo.
10 Atatero Mika anamuuza kuti: “Ukhale ndi ine ndipo uzitumikira ngati tate+ ndi wansembe+ wanga. Ine ndizikupatsa ndalama zasiliva 10 pa chaka, komanso zovala zako zoyenera ndi chakudya.” Pamenepo Mleviyo analowa m’nyumbamo.