Oweruza 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Poyankha iye anati: “Mika anagwirizana ndi ine kuti andilembe ntchito,+ ndi cholinga choti ndizitumikira monga wansembe+ wake.” Oweruza 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ana a Dani anatenga zimene Mika anapanga komanso wansembe+ wake, ndipo anapitiriza ulendo wawo wa ku Laisi+ kukaukira anthu aphee ndi osatekeseka.+ Atafika kumeneko anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kutentha mzindawo ndi moto.+ Mika 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atsogoleri a mumzindawo saweruza asanalandire chiphuphu+ ndipo ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro.+ Aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+ Komatu iwo amadalira Yehova ndipo amanena kuti: “Kodi Yehova sali pakati pathu?+ Choncho tsoka silidzatigwera.”+
4 Poyankha iye anati: “Mika anagwirizana ndi ine kuti andilembe ntchito,+ ndi cholinga choti ndizitumikira monga wansembe+ wake.”
27 Ana a Dani anatenga zimene Mika anapanga komanso wansembe+ wake, ndipo anapitiriza ulendo wawo wa ku Laisi+ kukaukira anthu aphee ndi osatekeseka.+ Atafika kumeneko anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kutentha mzindawo ndi moto.+
11 Atsogoleri a mumzindawo saweruza asanalandire chiphuphu+ ndipo ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro.+ Aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+ Komatu iwo amadalira Yehova ndipo amanena kuti: “Kodi Yehova sali pakati pathu?+ Choncho tsoka silidzatigwera.”+