Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Dani adzaweruza anthu a mtundu wake monga mmodzi wa mafuko a Isiraeli.+

  • Oweruza 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Zikatero, Yehova anali kuwapatsa oweruza,+ ndipo anali kuwapulumutsa m’manja mwa ofunkha.+

  • Oweruza 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano ana a Isiraeli anayambiranso kuchita zoipa pamaso pa Yehova,+ moti Yehova anawapereka m’manja mwa Afilisiti+ zaka 40.

  • Oweruza 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna. M’mutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri+ wa Mulungu potuluka m’mimba.+ Iye adzakhala patsogolo populumutsa Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+

  • Oweruza 16:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kenako abale ake ndi anthu onse a m’nyumba ya bambo ake, anapita kumeneko kukatenga mtembo wa Samisoni ndi kubwera nawo kwawo, ndipo anamuika m’manda a bambo ake Manowa,+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli.+ Samisoni anali ataweruza Isiraeli zaka 20.+

  • Nehemiya 9:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Chifukwa chochita zimenezi, munawapereka m’manja mwa adani awo+ amene anapitiriza kuwasautsa.+ Koma akakumana ndi nsautso, anali kukulirirani,+ ndipo inu munali kumva muli kumwambako.+ Chifukwa cha chifundo chanu chachikulu,+ munali kuwapatsa owapulumutsa+ amene anali kuwalanditsa m’manja mwa adani awo.+

  • Aheberi 11:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Nanga ndinenenso chiyani pamenepa? Nthawi indichepera kuti ndipitirize kufotokoza za Gidiyoni,+ Baraki,+ Samisoni,+ Yefita,+ Davide,+ komanso Samueli+ ndi aneneri enanso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena