Oweruza 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo Manowa anayamba kuchonderera Yehova kuti: “Yehova,+ lolani kuti munthu wa Mulungu woona amene munam’tuma, abwerenso kuti adzatilangize+ zoyenera kuchita ndi mwana amene adzabadweyo.”+
8 Pamenepo Manowa anayamba kuchonderera Yehova kuti: “Yehova,+ lolani kuti munthu wa Mulungu woona amene munam’tuma, abwerenso kuti adzatilangize+ zoyenera kuchita ndi mwana amene adzabadweyo.”+