Genesis 49:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Dani adzaweruza anthu a mtundu wake monga mmodzi wa mafuko a Isiraeli.+ Oweruza 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zikatero, Yehova anali kuwapatsa oweruza,+ ndipo anali kuwapulumutsa m’manja mwa ofunkha.+ Oweruza 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Samisoni anaweruza Isiraeli zaka 20 m’masiku a Afilisiti.+