Genesis 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ndili ndi ng’ombe, abulu, nkhosa, komanso antchito aamuna ndi aakazi.+ Ndatumiza amithenga kwa mbuyanga kukupemphani kuti mundikomere mtima.”’”+ Genesis 46:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ana amene Yosefe anabereka ku Iguputo analipo awiri. Onse a m’nyumba ya Yakobo amene anali nawo ku Iguputo analipo 70.+
5 Tsopano ndili ndi ng’ombe, abulu, nkhosa, komanso antchito aamuna ndi aakazi.+ Ndatumiza amithenga kwa mbuyanga kukupemphani kuti mundikomere mtima.”’”+
27 Ana amene Yosefe anabereka ku Iguputo analipo awiri. Onse a m’nyumba ya Yakobo amene anali nawo ku Iguputo analipo 70.+