Ekisodo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yosefe anali kale ku Iguputo.+ Anthu onse otuluka m’chiuno mwa Yakobo+ analipo 70. Deuteronomo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Makolo anu anapita ku Iguputo ndi anthu 70,+ ndipo tsopano Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ngati nyenyezi zakuthambo.+ Machitidwe 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero Yosefe anatumiza anthu ku Kanani kukatenga bambo ake Yakobo ndi achibale ake.+ Onse pamodzi analipo anthu 75.+
22 Makolo anu anapita ku Iguputo ndi anthu 70,+ ndipo tsopano Yehova Mulungu wanu wakuchulukitsani ngati nyenyezi zakuthambo.+
14 Chotero Yosefe anatumiza anthu ku Kanani kukatenga bambo ake Yakobo ndi achibale ake.+ Onse pamodzi analipo anthu 75.+