Genesis 46:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ana amene Yosefe anabereka ku Iguputo analipo awiri. Onse a m’nyumba ya Yakobo amene anali nawo ku Iguputo analipo 70.+ Ekisodo 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yosefe anali kale ku Iguputo.+ Anthu onse otuluka m’chiuno mwa Yakobo+ analipo 70. Machitidwe 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero Yosefe anatumiza anthu ku Kanani kukatenga bambo ake Yakobo ndi achibale ake.+ Onse pamodzi analipo anthu 75.+
27 Ana amene Yosefe anabereka ku Iguputo analipo awiri. Onse a m’nyumba ya Yakobo amene anali nawo ku Iguputo analipo 70.+
14 Chotero Yosefe anatumiza anthu ku Kanani kukatenga bambo ake Yakobo ndi achibale ake.+ Onse pamodzi analipo anthu 75.+