Genesis 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Udzalowe nazo ziwiriziwiri za mtundu uliwonse. Zolengedwa zouluka monga mwa mitundu yawo, nyama zoweta monga mwa mitundu yawo,+ nyama zonse zokwawa panthaka monga mwa mitundu yawo, kuti zidzasungike zamoyo.+ Levitiko 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndi mtundu uliwonse wa khwangwala.+ 1 Mafumu 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Uzikamwa+ madzi mumtsinje umene uli m’chigwacho, ndipo ndidzalamula akhwangwala+ kuti azikakupatsa chakudya.”+ Yobu 38:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?
20 Udzalowe nazo ziwiriziwiri za mtundu uliwonse. Zolengedwa zouluka monga mwa mitundu yawo, nyama zoweta monga mwa mitundu yawo,+ nyama zonse zokwawa panthaka monga mwa mitundu yawo, kuti zidzasungike zamoyo.+
4 Uzikamwa+ madzi mumtsinje umene uli m’chigwacho, ndipo ndidzalamula akhwangwala+ kuti azikakupatsa chakudya.”+
41 Ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?