Genesis 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo Nowa analowa m’chingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake, ndi akazi a ana ake. Iwo analowamo madzi achigumula asanayambe.+ 1 Petulo 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 imene inali yosamvera+ pa nthawi imene Mulungu anali kuleza mtima+ m’masiku a Nowa, pamene chingalawa chinali kupangidwa,+ chimene chinapulumutsa pamadzi anthu owerengeka, miyoyo 8 yokha.+ 2 Petulo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anaperekanso chilango padziko lakale lija ndipo sanalilekerere,+ koma anasunga Nowa, mlaliki wa chilungamo,+ pomupulumutsa pamodzi ndi anthu ena 7,+ pamene anabweretsa chigumula+ padziko la anthu osaopa Mulungu.
7 Pamenepo Nowa analowa m’chingalawacho, limodzi ndi ana ake aamuna, mkazi wake, ndi akazi a ana ake. Iwo analowamo madzi achigumula asanayambe.+
20 imene inali yosamvera+ pa nthawi imene Mulungu anali kuleza mtima+ m’masiku a Nowa, pamene chingalawa chinali kupangidwa,+ chimene chinapulumutsa pamadzi anthu owerengeka, miyoyo 8 yokha.+
5 Anaperekanso chilango padziko lakale lija ndipo sanalilekerere,+ koma anasunga Nowa, mlaliki wa chilungamo,+ pomupulumutsa pamodzi ndi anthu ena 7,+ pamene anabweretsa chigumula+ padziko la anthu osaopa Mulungu.