Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Kenako Mulungu anati: “M’madzi mukhale zamoyo zambirimbiri,+ ndiponso zolengedwa zouluka ziuluke m’mlengalenga mwa dziko lapansi.”+

  • Genesis 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Yehova Mulungu anali kuumba ndi dothi nyama iliyonse yakutchire, ndi cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga. Ndipo anayamba kuzibweretsa kwa munthuyo, kuti chilichonse achitche dzina. Dzina lililonse limene munthuyo anatchula chamoyo chilichonse,+ limenelo linakhaladi dzina lake.+

  • Genesis 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Udzalowe nazo ziwiriziwiri za mtundu uliwonse. Zolengedwa zouluka monga mwa mitundu yawo, nyama zoweta monga mwa mitundu yawo,+ nyama zonse zokwawa panthaka monga mwa mitundu yawo, kuti zidzasungike zamoyo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena