Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Mizinda yanu ndidzaiwononga ndi lupanga+ ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu,+ komanso sindidzalandira nsembe zanu zafungo lokhazika mtima pansi.+

  • Ezekieli 20:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Ndikadzakutulutsani pakati pa anthu a mitundu ina ndi kukusonkhanitsani pamodzi kuchokera m’mayiko osiyanasiyana kumene munabalalikira,+ ndidzasangalala nanu chifukwa cha nsembe zanu zafungo lokhazika mtima pansi,+ ndipo ndidzakhala woyera chifukwa cha inu pamaso pa anthu a mitundu ina.’+

  • Aefeso 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 ndipo yendanibe m’chikondi,+ monganso Khristu anakukondani+ n’kudzipereka yekha chifukwa cha inu. Iye anadzipereka yekha monga chopereka+ ndiponso monga nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+

  • Aheberi 13:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Komanso, musaiwale kuchita zabwino+ ndi kugawana zinthu ndi ena, pakuti nsembe zotero Mulungu amakondwera nazo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena