1 Timoteyo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu amenewo adzaletsa anthu kukwatira,+ ndipo adzalamula anthu kusala zakudya zina+ zimene Mulungu anazilenga+ kuti anthu amene ali ndi chikhulupiriro ndiponso odziwa choonadi molondola azidya moyamikira.+
3 Anthu amenewo adzaletsa anthu kukwatira,+ ndipo adzalamula anthu kusala zakudya zina+ zimene Mulungu anazilenga+ kuti anthu amene ali ndi chikhulupiriro ndiponso odziwa choonadi molondola azidya moyamikira.+