Genesis 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+ Ekisodo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti chofunda chake n’chomwecho.+ Imeneyo ndi nsalu yake yakunja. Adzafunda chiyani pogona? Ndiyeno akandilirira, ine ndidzamumvera ndithu, chifukwa ndine wachifundo.+
34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+
27 Pakuti chofunda chake n’chomwecho.+ Imeneyo ndi nsalu yake yakunja. Adzafunda chiyani pogona? Ndiyeno akandilirira, ine ndidzamumvera ndithu, chifukwa ndine wachifundo.+