Salimo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wosautsikayu anaitana ndipo Yehova anamva.+Anamupulumutsa m’masautso ake onse.+ Aefeso 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anachita zimenezi kuti mu nthawi* zimene zikubwera+ padzasonyezedwe chuma chopambana+ cha kukoma mtima kwake kwakukulu kumene anatisonyeza mogwirizana+ ndi Khristu Yesu.
7 Anachita zimenezi kuti mu nthawi* zimene zikubwera+ padzasonyezedwe chuma chopambana+ cha kukoma mtima kwake kwakukulu kumene anatisonyeza mogwirizana+ ndi Khristu Yesu.