Genesis 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma inuyo muberekane, muchuluke, mufalikire padziko lonse lapansi.”+ Genesis 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Atatuwa ndiwo anali ana a Nowa. Ndipo anthu onse amene ali padziko lapansi anachokera mwa iwowa.+ Machitidwe 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mtundu wonse wa anthu,+ kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anakhazikitsa nthawi zoikidwiratu+ komanso anaika malire achikhalire a malo oti anthu azikhala.+
26 Ndipo kuchokera mwa munthu mmodzi+ anapanga mtundu wonse wa anthu,+ kuti akhale padziko lonse lapansi.+ Iye anakhazikitsa nthawi zoikidwiratu+ komanso anaika malire achikhalire a malo oti anthu azikhala.+