Genesis 24:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yehova wamudalitsa kwambiri mbuyanga moti akum’lemeretsabe pomupatsa nkhosa, ng’ombe, siliva, golide, antchito aamuna ndi aakazi, ngamila ndi abulu.+ Deuteronomo 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzikumbukira Yehova Mulungu wanu, chifukwa ndiye amakupatsani mphamvu kuti mupeze chuma,+ pofuna kusunga pangano lake limene analumbirira makolo anu, monga mmene wachitira lero.+
35 Yehova wamudalitsa kwambiri mbuyanga moti akum’lemeretsabe pomupatsa nkhosa, ng’ombe, siliva, golide, antchito aamuna ndi aakazi, ngamila ndi abulu.+
18 Muzikumbukira Yehova Mulungu wanu, chifukwa ndiye amakupatsani mphamvu kuti mupeze chuma,+ pofuna kusunga pangano lake limene analumbirira makolo anu, monga mmene wachitira lero.+