Salimo 127:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+ Miyambo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Madalitso a Yehova ndi amene amalemeretsa,+ ndipo sawonjezerapo ululu.+ Hoseya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iye sanavomereze+ kuti ndine amene ndinali kumupatsa mbewu,+ vinyo wotsekemera* ndi mafuta. Sanavomerezenso kuti ndine amene ndinamuchulukitsira siliva ndi golide amene iye anali kumugwiritsa ntchito popembedza Baala.+
127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+Yehova akapanda kulondera mzinda,+Alonda amakhala maso pachabe.+
8 Koma iye sanavomereze+ kuti ndine amene ndinali kumupatsa mbewu,+ vinyo wotsekemera* ndi mafuta. Sanavomerezenso kuti ndine amene ndinamuchulukitsira siliva ndi golide amene iye anali kumugwiritsa ntchito popembedza Baala.+