Genesis 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abulamu anali ndi chuma chambiri. Anali ndi ziweto, siliva ndi golide.+ Salimo 107:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mulungu amawadalitsa moti amachuluka kwambiri,+Ndipo salola kuti ng’ombe zawo zikhale zochepa.+