Genesis 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’kupita kwa nthawi, anasamuka pamalopo n’kupita kudera lamapiri, kum’mawa kwa Beteli.+ Kumeneko iye anamanga hema wake. Beteli anali kumadzulo kwake ndipo Ai+ anali kum’mawa kwake. Kenako anamangira Yehova guwa lansembe,+ n’kuyamba kuitana pa dzina la Yehova.+ Yoswa 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano Yoswa anatumiza amuna ena kuchokera ku Yeriko kupita ku Ai,+ pafupi ndi Beti-aveni,+ kum’mawa kwa Beteli.+ Iye anawauza kuti: “Pitani kumeneko, mukazonde dzikolo.” Amunawo anapita, n’kukazonda dziko la Ai.+
8 M’kupita kwa nthawi, anasamuka pamalopo n’kupita kudera lamapiri, kum’mawa kwa Beteli.+ Kumeneko iye anamanga hema wake. Beteli anali kumadzulo kwake ndipo Ai+ anali kum’mawa kwake. Kenako anamangira Yehova guwa lansembe,+ n’kuyamba kuitana pa dzina la Yehova.+
2 Tsopano Yoswa anatumiza amuna ena kuchokera ku Yeriko kupita ku Ai,+ pafupi ndi Beti-aveni,+ kum’mawa kwa Beteli.+ Iye anawauza kuti: “Pitani kumeneko, mukazonde dzikolo.” Amunawo anapita, n’kukazonda dziko la Ai.+