Genesis 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Farao anamusamalira bwino Abulamu chifukwa cha mkazi wake, moti anamupatsa nkhosa, ng’ombe ndi abulu. Anamupatsanso antchito aamuna ndi aakazi, komanso abulu aakazi ndi ngamila.+ Agalatiya 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano, Hagara ameneyu akutanthauza Sinai,+ phiri la ku Arabiya, ndipo masiku ano akufanana ndi Yerusalemu, pakuti ali mu ukapolo+ pamodzi ndi ana ake.
16 Farao anamusamalira bwino Abulamu chifukwa cha mkazi wake, moti anamupatsa nkhosa, ng’ombe ndi abulu. Anamupatsanso antchito aamuna ndi aakazi, komanso abulu aakazi ndi ngamila.+
25 Tsopano, Hagara ameneyu akutanthauza Sinai,+ phiri la ku Arabiya, ndipo masiku ano akufanana ndi Yerusalemu, pakuti ali mu ukapolo+ pamodzi ndi ana ake.