Genesis 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nyamuka! Dzutsa mnyamatayo, ndipo umugwirizize ndi dzanja lako, chifukwa ndidzamupangitsa kukhala mtundu waukulu.”+ 1 Mbiri 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Awa ndiwo mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+
18 Nyamuka! Dzutsa mnyamatayo, ndipo umugwirizize ndi dzanja lako, chifukwa ndidzamupangitsa kukhala mtundu waukulu.”+