17 Anthu otsala pa amuna oponya mivi ndi uta, omwe ndi amuna amphamvu a ana a Kedara, adzakhala ochepa,+ pakuti Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena zimenezi.”+
21 Unalemba ntchito Aluya+ ndi atsogoleri onse a ku Kedara+ kuti azikugulitsira malonda. Iwo anali kukugulitsira ana a nkhosa amphongo, nkhosa zamphongo ndi mbuzi zamphongo.+