Yeremiya 49:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ponena za Kedara+ ndi maufumu a Hazori+ amene Nebukadirezara mfumu ya Babulo anawapha,+ Yehova wanena kuti: “Nyamukani amuna inu, pitani ku Kedara ndipo mukafunkhe zinthu za ana a Kum’mawa.+
28 Ponena za Kedara+ ndi maufumu a Hazori+ amene Nebukadirezara mfumu ya Babulo anawapha,+ Yehova wanena kuti: “Nyamukani amuna inu, pitani ku Kedara ndipo mukafunkhe zinthu za ana a Kum’mawa.+