Genesis 24:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Munthuyo atamva zimenezo, anapita n’kukalowa m’nyumbamo. Pamenepo Labani anamasula ngamila ndi kuzipatsa chakudya. Anatenganso madzi n’kusambitsa mapazi a mlendoyo ndi mapazi a anyamata omwe iye anali nawo.+ 1 Samueli 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Nthawi yomweyo, ananyamuka ndi kugwada mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Ine kapolo wanu ndine wokonzeka kukhala mtumiki wosambitsa mapazi+ a atumiki a mbuyanga.”+ Yohane 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atatero anathira madzi m’beseni ndi kuyamba kusambitsa mapazi+ a ophunzira ndi kuwapukuta ndi thaulo limene anamanga m’chiuno lija.
32 Munthuyo atamva zimenezo, anapita n’kukalowa m’nyumbamo. Pamenepo Labani anamasula ngamila ndi kuzipatsa chakudya. Anatenganso madzi n’kusambitsa mapazi a mlendoyo ndi mapazi a anyamata omwe iye anali nawo.+
41 Nthawi yomweyo, ananyamuka ndi kugwada mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Ine kapolo wanu ndine wokonzeka kukhala mtumiki wosambitsa mapazi+ a atumiki a mbuyanga.”+
5 Atatero anathira madzi m’beseni ndi kuyamba kusambitsa mapazi+ a ophunzira ndi kuwapukuta ndi thaulo limene anamanga m’chiuno lija.