Genesis 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tiye, fulumira! Thawira kumeneko, ndipo sindichita kanthu mpaka utafika kumeneko.”+ N’chifukwa chake iye anatcha mzindawo dzina lakuti Zowari.*+
22 Tiye, fulumira! Thawira kumeneko, ndipo sindichita kanthu mpaka utafika kumeneko.”+ N’chifukwa chake iye anatcha mzindawo dzina lakuti Zowari.*+