Genesis 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele,+ Msiriya+ wa ku Padana-ramu, mlongo wake wa Labani, Msiriya. Genesis 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yakobo ataona Rakele mwana wa Labani, mlongo wa mayi ake, ndiponso nkhosa za Labaniyo, nthawi yomweyo anapita pachitsime paja, n’kugubuduza mwalawo kuuchotsa pachitsimepo. Atatero anatungira madzi nkhosa za Labani, mlongo wa mayi ake.+
20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele,+ Msiriya+ wa ku Padana-ramu, mlongo wake wa Labani, Msiriya.
10 Yakobo ataona Rakele mwana wa Labani, mlongo wa mayi ake, ndiponso nkhosa za Labaniyo, nthawi yomweyo anapita pachitsime paja, n’kugubuduza mwalawo kuuchotsa pachitsimepo. Atatero anatungira madzi nkhosa za Labani, mlongo wa mayi ake.+