Deuteronomo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Musadye nyama iliyonse imene mwaipeza yakufa.+ Muziipereka kwa mlendo wokhala mumzinda wanu kuti adye, kapena muziigulitsa kwa mlendo* chifukwa inu ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. “Musawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi wake.+ Miyambo 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wolungama amasamalira moyo wa chiweto chake,+ koma chisamaliro cha anthu oipa n’chankhanza.+
21 “Musadye nyama iliyonse imene mwaipeza yakufa.+ Muziipereka kwa mlendo wokhala mumzinda wanu kuti adye, kapena muziigulitsa kwa mlendo* chifukwa inu ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. “Musawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi wake.+