Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pagulu lawo, moyo wanga usakhale nawo.+ Maganizo anga asagwirizane ndi mpingo wawo,+ chifukwa atakwiya anapha anthu,+ ndipo mwankhanza zawo, anapundula* ng’ombe zamphongo.

  • Oweruza 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zitatero, Adoni-bezeki anati: “Panali mafumu 70 odulidwa zala zamanthu za m’manja ndi zala zazikulu za kumapazi, amene anali kutola chakudya pansi pa tebulo langa. Mulungu wandibwezera zimene ndinachita.”+ Kenako anam’tengera ku Yerusalemu+ kumene anakafera.

  • 1 Samueli 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Nahasi Muamoni ananena kuti: “Ndidzachita nanu pangano pokhapokha nditaboola diso+ la kudzanja lamanja la aliyense wa inu, kuti chikhale chinthu chotonzetsa Aisiraeli onse.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena