Ekisodo 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mose ali m’phirimo, anthu anaona kuti akuchedwa kutsika.+ Chotero anthuwo anasonkhana kwa Aroni ndi kumuuza kuti: “Tipangire mulungu woti atitsogolere,+ chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitulutsa m’dziko la Iguputo.”+
32 Mose ali m’phirimo, anthu anaona kuti akuchedwa kutsika.+ Chotero anthuwo anasonkhana kwa Aroni ndi kumuuza kuti: “Tipangire mulungu woti atitsogolere,+ chifukwa sitikudziwa zimene zachitikira Mose, amene anatitulutsa m’dziko la Iguputo.”+