Ekisodo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Upangenso mitengo yonyamulira ya mtengo wa mthethe ndipo uikute ndi golide.+ 1 Mbiri 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno ana a Alevi anakanyamula+ likasa la Mulungu woona, monga mmene Mose anawalamulira potsatira mawu a Yehova. Iwo analinyamula pamapewa awo pogwiritsa ntchito ndodo zake.+
15 Ndiyeno ana a Alevi anakanyamula+ likasa la Mulungu woona, monga mmene Mose anawalamulira potsatira mawu a Yehova. Iwo analinyamula pamapewa awo pogwiritsa ntchito ndodo zake.+