Genesis 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero anam’pitikitsa munthuyo. Ndiyeno anaika akerubi+ kum’mawa kwa munda wa Edeniwo.+ Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linali kuzungulira mosalekeza, kutchinga njira yopita ku mtengo wa moyo.
24 Chotero anam’pitikitsa munthuyo. Ndiyeno anaika akerubi+ kum’mawa kwa munda wa Edeniwo.+ Anaikanso lupanga loyaka moto, limene linali kuzungulira mosalekeza, kutchinga njira yopita ku mtengo wa moyo.