Ekisodo 37:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfundo imodzi inali pansi pa nthambi zake ziwiri, mfundo ina inalinso pansi pa nthambi zake ziwiri, ndipo mfundo inanso inali pansi pa nthambi zinanso ziwiri. Zinali choncho ndi nthambi 6 zotuluka m’choikapo nyale.+
21 Mfundo imodzi inali pansi pa nthambi zake ziwiri, mfundo ina inalinso pansi pa nthambi zake ziwiri, ndipo mfundo inanso inali pansi pa nthambi zinanso ziwiri. Zinali choncho ndi nthambi 6 zotuluka m’choikapo nyale.+