Ekisodo 25:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mfundo imodzi ikhale pansi pa nthambi zake ziwiri, mfundo ina ikhalenso pansi pa nthambi zake ziwiri, ndipo mfundo inanso ikhale pansi pa nthambi zinanso ziwiri. Zikhale choncho ndi nthambi 6 zotuluka m’choikapo nyale.+
35 Mfundo imodzi ikhale pansi pa nthambi zake ziwiri, mfundo ina ikhalenso pansi pa nthambi zake ziwiri, ndipo mfundo inanso ikhale pansi pa nthambi zinanso ziwiri. Zikhale choncho ndi nthambi 6 zotuluka m’choikapo nyale.+