Ekisodo 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumbali yakumpoto, mpandawo unali mikono 100 kutalika kwake. Nsanamira zake 20 ndi zitsulo 20 zokhazikapo nsanamirazo zinali zamkuwa. Tizitsulo ta nsanamira tokolowekapo nsalu ndi tizitsulo tolumikizira tinali tasiliva.+
11 Kumbali yakumpoto, mpandawo unali mikono 100 kutalika kwake. Nsanamira zake 20 ndi zitsulo 20 zokhazikapo nsanamirazo zinali zamkuwa. Tizitsulo ta nsanamira tokolowekapo nsalu ndi tizitsulo tolumikizira tinali tasiliva.+