Chivumbulutso 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wokhala pampandoyo, anali wooneka+ ngati mwala wa yasipi,+ ndi mwala wofiira wamtengo wapatali. Utawaleza+ wooneka ngati mwala wa emarodi+ unazungulira mpando wachifumuwo. Chivumbulutso 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 uli ndi ulemerero wa Mulungu.+ Unali wonyezimira ngati mwala wamtengo wapatali kwambiri, ngati mwala wa yasipi wowala mbee! ngati galasi.+
3 Wokhala pampandoyo, anali wooneka+ ngati mwala wa yasipi,+ ndi mwala wofiira wamtengo wapatali. Utawaleza+ wooneka ngati mwala wa emarodi+ unazungulira mpando wachifumuwo.
11 uli ndi ulemerero wa Mulungu.+ Unali wonyezimira ngati mwala wamtengo wapatali kwambiri, ngati mwala wa yasipi wowala mbee! ngati galasi.+