Ekisodo 39:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo malaya odula manjawo anali otsegula pamwamba pake, pakatikati, ngati chovala cha kunkhondo chamamba achitsulo. Potsegulapo panali popenderera m’mphepete mwake kuti pasang’ambike.+
23 Ndipo malaya odula manjawo anali otsegula pamwamba pake, pakatikati, ngati chovala cha kunkhondo chamamba achitsulo. Potsegulapo panali popenderera m’mphepete mwake kuti pasang’ambike.+