Ekisodo 28:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Malayawo akhale otsegula pamwamba pake, pakatikati. Potsegulapo pakhale popenderera m’mphepete mwake ndi nsalu yowomba. Pakhale potsegula ngati chovala cha kunkhondo chamamba achitsulo, kuti pasang’ambike.+
32 Malayawo akhale otsegula pamwamba pake, pakatikati. Potsegulapo pakhale popenderera m’mphepete mwake ndi nsalu yowomba. Pakhale potsegula ngati chovala cha kunkhondo chamamba achitsulo, kuti pasang’ambike.+