Ekisodo 29:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Aroni ndi ana akewo uwamange malamba a pamimba. Ana akewo uwakulunge mipango kumutu kwawo ndipo unsembe udzakhala wawo. Limeneli ndi lamulo langa mpaka kalekale.+ Choncho upatse Aroni ndi ana ake mphamvu. + Levitiko 8:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7,+ kufikira tsiku lomaliza la kulongedwa kwanu unsembe, chifukwa kukupatsani mphamvu* kudzatenga masiku 7.+ Numeri 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amenewa ndiwo anali mayina a ana a Aroni. Iwo anali ansembe odzozedwa amene anapatsidwa mphamvu* yotumikira monga ansembe.+
9 Ndiyeno Aroni ndi ana akewo uwamange malamba a pamimba. Ana akewo uwakulunge mipango kumutu kwawo ndipo unsembe udzakhala wawo. Limeneli ndi lamulo langa mpaka kalekale.+ Choncho upatse Aroni ndi ana ake mphamvu. +
33 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kwa masiku 7,+ kufikira tsiku lomaliza la kulongedwa kwanu unsembe, chifukwa kukupatsani mphamvu* kudzatenga masiku 7.+
3 Amenewa ndiwo anali mayina a ana a Aroni. Iwo anali ansembe odzozedwa amene anapatsidwa mphamvu* yotumikira monga ansembe.+