Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 7:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Nganga ya nsembe yoweyula+ ndiponso mwendo, umene ndi gawo lopatulika, ndikuzitenga pansembe zachiyanjano za ana a Isiraeli. Ndikuzitenga kwa ana a Isiraeli ndi kuzipereka kwa Aroni wansembe ndi ana ake. Ili ndi lamulo mpaka kalekale.

  • Levitiko 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mudyenso nganga ya nsembe yoweyula,*+ ndi mwendo umene ndi gawo lopatulika.+ Muzidyere m’malo oyera, inuyo, ana anu aamuna ndi ana anu aakazi.+ Muyenera kutero chifukwa zapatsidwa kwa inu monga gawo lanu ndi gawo la ana anu kuchokera pa nsembe zachiyanjano za ana a Isiraeli.

  • Numeri 15:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 muzikapereka chopereka kwa Yehova pachakudya chilichonse cha m’dzikolo,+ chimene muzikadya.

  • Numeri 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Chakhumi chimene ana a Isiraeli azipereka kwa Yehova monga chopereka, ndawapatsa Alevi monga cholowa chawo. N’chifukwa chake ndinawauza kuti, ‘Asalandire cholowa pakati pa ana a Isiraeli.’”+

  • Deuteronomo 18:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Ndipo izi ndi zinthu zimene ansembe ayenera kulandira kuchokera kwa anthu. Amene akupereka nsembe ya ng’ombe kapena nkhosa, azipereka kwa wansembe mwendo wakutsogolo, nsagwada ndi chifu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena