Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “Kenako utenge nganga ya nkhosa yolongera Aroni unsembe,+ ndi kuiweyulira uku ndi uku monga nsembe yoweyula yoperekedwa kwa Yehova. Imeneyo ikhale gawo lako.

  • Levitiko 7:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiyeno wansembe azitentha mafutawo+ paguwa lansembe, koma ngangayo izikhala ya Aroni ndi ana ake.+

  • Levitiko 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Koma Aroni anaweyula*+ cha uku ndi uku ngangazo ndi mwendo wakumbuyo wa kudzanja lamanja pamaso pa Yehova, monga mmene Mose analamulira.

  • Numeri 18:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mphatso zonse za ana a Isiraeli, limodzi ndi nsembe zawo zonse zoweyula*+ zimene azipereka monga zopereka zawo,+ zizikhala zako. Ndazipereka kwa iwe ndi kwa ana ako aamuna, limodzi ndi ana ako aakazi.+ Zikhale gawo lanu mpaka kalekale. Aliyense wa m’nyumba yako amene ndi wosadetsedwa azidya nawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena