Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Akatero azituluka ndi kupita kuguwa lansembe+ limene lili pamaso pa Yehova kuti akaliphimbire machimo. Ndiyeno azitenga ena mwa magazi a ng’ombe yamphongo ndi a mbuzi n’kuwapaka panyanga zonse za guwa lansembe.+

  • Levitiko 23:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Tsiku la 10 m’mwezi wa 7 umenewu ndi tsiku la mwambo wophimba machimo.+ Muzichita msonkhano wopatulika ndipo muzidzisautsa*+ ndi kupereka nsembe+ yotentha ndi moto kwa Yehova.

  • Aheberi 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma m’chipinda chachiwiricho, mkulu wa ansembe yekha ndiye anali kulowamo kamodzi pa chaka,+ ndipo sanali kulowamo popanda kutenga magazi.+ Magaziwo anali kuwapereka chifukwa cha iye mwini,+ komanso chifukwa cha machimo a anthu amene anachita mosadziwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena