Ekisodo 38:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwamuna aliyense amene anawerengedwa, kuyambira wa zaka 20 kupita m’tsogolo,+ anapereka hafu ya sekeli lolingana ndi hafu ya sekeli la kumalo oyera. Owerengedwa onse anakwana 603,550.+ Numeri 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uwerenge kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ aliyense woyenerera kupita kunkhondo pakati pa Aisiraeli.+ Iweyo ndi Aroni muwalembe m’kaundula malinga ndi magulu awo a asilikali. Numeri 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Werengani amuna onse oyenera kupita kunkhondo pakati pa khamu lonse la ana a Isiraeli. Muwerenge kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, potsata nyumba za makolo awo.”+
26 Mwamuna aliyense amene anawerengedwa, kuyambira wa zaka 20 kupita m’tsogolo,+ anapereka hafu ya sekeli lolingana ndi hafu ya sekeli la kumalo oyera. Owerengedwa onse anakwana 603,550.+
3 Uwerenge kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo,+ aliyense woyenerera kupita kunkhondo pakati pa Aisiraeli.+ Iweyo ndi Aroni muwalembe m’kaundula malinga ndi magulu awo a asilikali.
2 “Werengani amuna onse oyenera kupita kunkhondo pakati pa khamu lonse la ana a Isiraeli. Muwerenge kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, potsata nyumba za makolo awo.”+